Ekisodo 15:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kenako Miriamu, mneneri wamkazi, mlongo wake wa Aroni,+ anatenga maseche m’manja mwake,+ ndipo akazi ena onse anam’tsatira akuimba maseche ndi kuvina.+ Salimo 30:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mwasintha kulira kwanga kuti kukhale kuvina.+Mwandivula chiguduli* changa ndipo mwandiveka chisangalalo,+
20 Kenako Miriamu, mneneri wamkazi, mlongo wake wa Aroni,+ anatenga maseche m’manja mwake,+ ndipo akazi ena onse anam’tsatira akuimba maseche ndi kuvina.+
11 Mwasintha kulira kwanga kuti kukhale kuvina.+Mwandivula chiguduli* changa ndipo mwandiveka chisangalalo,+