Salimo 96:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pakuti iye wabwera.+Iye wabwera kudzaweruza dziko lapansi.+Adzaweruza dziko mwachilungamo,+Ndipo adzaweruza mitundu ya anthu mokhulupirika.+
13 Pakuti iye wabwera.+Iye wabwera kudzaweruza dziko lapansi.+Adzaweruza dziko mwachilungamo,+Ndipo adzaweruza mitundu ya anthu mokhulupirika.+