1 Mbiri 14:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndiyeno Hiramu+ mfumu ya Turo+ anatumiza amithenga kwa Davide. Anatumizanso matabwa a mkungudza,+ anthu omanga makoma, ndi anthu a ntchito zamatabwa kuti akamangire Davide nyumba.+
14 Ndiyeno Hiramu+ mfumu ya Turo+ anatumiza amithenga kwa Davide. Anatumizanso matabwa a mkungudza,+ anthu omanga makoma, ndi anthu a ntchito zamatabwa kuti akamangire Davide nyumba.+