Aefeso 3:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Tsopano kwa iye amene angathe kuchita zazikulu kwambiri kuposa zonse zimene timapempha kapena kuganiza,+ malinga ndi mphamvu yake imene ikugwira ntchito+ mwa ife,
20 Tsopano kwa iye amene angathe kuchita zazikulu kwambiri kuposa zonse zimene timapempha kapena kuganiza,+ malinga ndi mphamvu yake imene ikugwira ntchito+ mwa ife,