Yeremiya 31:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 “Pa nthawi imeneyo ndidzakhala Mulungu wa mabanja onse a Isiraeli, ndipo iwo adzakhala anthu anga,”+ watero Yehova. Aheberi 11:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma tsopano akufunitsitsa malo abwino koposa, amene ndi malo akumwamba.+ Pa chifukwa chimenechi, Mulungu sachita nawo manyazi kuti azimuitana monga Mulungu wawo,+ pakuti iye wawakonzera mzinda.+
31 “Pa nthawi imeneyo ndidzakhala Mulungu wa mabanja onse a Isiraeli, ndipo iwo adzakhala anthu anga,”+ watero Yehova.
16 Koma tsopano akufunitsitsa malo abwino koposa, amene ndi malo akumwamba.+ Pa chifukwa chimenechi, Mulungu sachita nawo manyazi kuti azimuitana monga Mulungu wawo,+ pakuti iye wawakonzera mzinda.+