Salimo 35:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Adani anga amandibwezera zoipa m’malo mwa zabwino,+Ndipo ndimakhala wachisoni ngati wofedwa.+