2 Samueli 10:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyeno ana a Amoni anapita kukafola mwa dongosolo lomenyera nkhondo kuchipata cha mzinda. Nawonso Asiriya a ku Zoba, a ku Rehobu,+ a ku Isitobu ndi a ku Maaka anafola paokha kutchire.+
8 Ndiyeno ana a Amoni anapita kukafola mwa dongosolo lomenyera nkhondo kuchipata cha mzinda. Nawonso Asiriya a ku Zoba, a ku Rehobu,+ a ku Isitobu ndi a ku Maaka anafola paokha kutchire.+