Mlaliki 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Awiri amaposa mmodzi,+ chifukwa amapeza mphoto yabwino pa ntchito yawo imene amaigwira mwakhama.+