Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 17:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Mtengo wa mkondo wake unali waukulu ngati mtanda wa owomba nsalu,+ ndipo mutu wachitsulo wa mkondowo unali wolemera masekeli 600. Munthu womunyamulira chishango chake chachikulu anali kuyenda patsogolo pake.

  • 1 Mbiri 11:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Benaya ndiye anaphanso Mwiguputo wa msinkhu waukulu modabwitsa, yemwe anali chiphona chachitali mikono* isanu.+ Mwiguputoyo anali ndi mkondo+ m’manja mwake, waukulu ngati mtanda wa owomba nsalu, koma Benaya anapitabe kukakumana naye atanyamula ndodo, n’kulanda mkondowo ndipo anamupha ndi mkondo wake womwewo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena