1 Mafumu 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Panopa ndikuganiza zomanga nyumba ya dzina la Yehova Mulungu wanga,+ monga momwe Yehova analonjezera Davide bambo anga kuti, ‘Mwana wako amene ndidzamuike pampando wako wachifumu m’malo mwa iweyo, ndi amene adzamange nyumba ya dzina langa.’+ 1 Mbiri 17:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Iye ndiye adzandimangire nyumba,+ ndipo ndithu ndidzakhazikitsa mpando wake wachifumu mpaka kalekale.+
5 Panopa ndikuganiza zomanga nyumba ya dzina la Yehova Mulungu wanga,+ monga momwe Yehova analonjezera Davide bambo anga kuti, ‘Mwana wako amene ndidzamuike pampando wako wachifumu m’malo mwa iweyo, ndi amene adzamange nyumba ya dzina langa.’+
12 Iye ndiye adzandimangire nyumba,+ ndipo ndithu ndidzakhazikitsa mpando wake wachifumu mpaka kalekale.+