1 Mbiri 28:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Anam’patsanso malangizo okhudza magulu+ a ansembe ndi a Alevi, ntchito yonse yokhudza utumiki wa panyumba ya Yehova, ndiponso malangizo okhudza ziwiya zonse za utumiki wa panyumba ya Yehova.
13 Anam’patsanso malangizo okhudza magulu+ a ansembe ndi a Alevi, ntchito yonse yokhudza utumiki wa panyumba ya Yehova, ndiponso malangizo okhudza ziwiya zonse za utumiki wa panyumba ya Yehova.