Levitiko 7:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “‘Nsembe iliyonse yambewu imene ingaphikidwe mu uvuni,+ iliyonse yophika mu mphika wa mafuta ambiri+ ndiponso yophika m’chiwaya+ izikhala ya wansembe amene wapereka nsembeyo. Ndithu izikhala yake.+
9 “‘Nsembe iliyonse yambewu imene ingaphikidwe mu uvuni,+ iliyonse yophika mu mphika wa mafuta ambiri+ ndiponso yophika m’chiwaya+ izikhala ya wansembe amene wapereka nsembeyo. Ndithu izikhala yake.+