Levitiko 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “‘Ngati mukupereka nsembe yambewu yophika m’chiwaya,+ izikhala ya ufa wabwino kwambiri wothira mafuta, yopanda chofufumitsa. Levitiko 6:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Nsembeyo ikhale yosakaniza ndi mafuta, yophika m’chiwaya.+ Ikhale yosakaniza bwino ndi mafuta. Upereke mitanda ya nsembe yambewu monga fungo lokhazika mtima pansi kwa Yehova. 1 Mbiri 23:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Anali kutumidwanso pa ntchito zokhudza mkate wosanjikiza,+ ufa wosalala+ wa nsembe yambewu, mikate yopyapyala+ yopanda chofufumitsa,+ makeke ophika m’chiwaya,+ ufa wokanya wosakaniza ndi mafuta,+ ndiponso miyezo yosiyanasiyana.+
5 “‘Ngati mukupereka nsembe yambewu yophika m’chiwaya,+ izikhala ya ufa wabwino kwambiri wothira mafuta, yopanda chofufumitsa.
21 Nsembeyo ikhale yosakaniza ndi mafuta, yophika m’chiwaya.+ Ikhale yosakaniza bwino ndi mafuta. Upereke mitanda ya nsembe yambewu monga fungo lokhazika mtima pansi kwa Yehova.
29 Anali kutumidwanso pa ntchito zokhudza mkate wosanjikiza,+ ufa wosalala+ wa nsembe yambewu, mikate yopyapyala+ yopanda chofufumitsa,+ makeke ophika m’chiwaya,+ ufa wokanya wosakaniza ndi mafuta,+ ndiponso miyezo yosiyanasiyana.+