1 Mbiri 9:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ena a iwo anali amuna osankhidwa kuti aziyang’anira ziwiya zina, ziwiya zonse zopatulika,+ ufa wosalala,+ vinyo,+ mafuta,+ lubani,*+ ndi mafuta a basamu.+
29 Ena a iwo anali amuna osankhidwa kuti aziyang’anira ziwiya zina, ziwiya zonse zopatulika,+ ufa wosalala,+ vinyo,+ mafuta,+ lubani,*+ ndi mafuta a basamu.+