19 Choncho funafunani Yehova Mulungu wanu+ ndi mtima wanu ndi moyo wanu.+ Yambani kumanga nyumba yopatulika+ ya Yehova Mulungu woona.+ Kenako mukatenge likasa+ la pangano la Yehova ndi ziwiya zopatulika za Mulungu woona n’kuziika m’nyumba ya dzina+ la Yehova imene imangidweyo.”