2 Mbiri 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ansembe achilevi+ ananyamula Likasa,+ chihema chokumanako,+ ndi ziwiya zonse zopatulika+ zimene zinali m’chihemacho.
5 Ansembe achilevi+ ananyamula Likasa,+ chihema chokumanako,+ ndi ziwiya zonse zopatulika+ zimene zinali m’chihemacho.