Ekisodo 40:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Mose sanathenso kulowa m’chihema chokumanako, chifukwa mtambo+ unaphimba chihemacho ndipo munadzaza ulemerero wa Yehova.+ Numeri 4:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Tsopano uyu ndi katundu amene azinyamula,+ monga gawo la utumiki wawo m’chihema chokumanako: Mafelemu+ a chihema chopatulika, mipiringidzo yake,+ mizati yake,+ ndiponso zitsulo zokhazikapo mizati ndi mafelemu.+
35 Mose sanathenso kulowa m’chihema chokumanako, chifukwa mtambo+ unaphimba chihemacho ndipo munadzaza ulemerero wa Yehova.+
31 Tsopano uyu ndi katundu amene azinyamula,+ monga gawo la utumiki wawo m’chihema chokumanako: Mafelemu+ a chihema chopatulika, mipiringidzo yake,+ mizati yake,+ ndiponso zitsulo zokhazikapo mizati ndi mafelemu.+