1 Mafumu 8:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iwo ananyamula Likasa la Yehova, chihema chokumanako+ komanso zinthu zonse zopatulika zimene zinali mʼchihemacho. Ansembe ndi Alevi anabweretsa zinthuzi.
4 Iwo ananyamula Likasa la Yehova, chihema chokumanako+ komanso zinthu zonse zopatulika zimene zinali mʼchihemacho. Ansembe ndi Alevi anabweretsa zinthuzi.