Ekisodo 40:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Pa tsiku loyamba la mwezi woyamba, udzamange chihema kapena kuti chihema chokumanako.+ 2 Mbiri 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Zitatero, Solomo anabwerera ku Yerusalemu kuchokera kumalo okwezeka ku Gibiyoni,+ kuchihema chokumanako, ndipo anapitiriza kulamulira Isiraeli.
13 Zitatero, Solomo anabwerera ku Yerusalemu kuchokera kumalo okwezeka ku Gibiyoni,+ kuchihema chokumanako, ndipo anapitiriza kulamulira Isiraeli.