Levitiko 6:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Nsembeyo ikhale yosakaniza ndi mafuta, yophika m’chiwaya.+ Ikhale yosakaniza bwino ndi mafuta. Upereke mitanda ya nsembe yambewu monga fungo lokhazika mtima pansi kwa Yehova. Levitiko 7:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “‘Nsembe iliyonse yambewu imene ingaphikidwe mu uvuni,+ iliyonse yophika mu mphika wa mafuta ambiri+ ndiponso yophika m’chiwaya+ izikhala ya wansembe amene wapereka nsembeyo. Ndithu izikhala yake.+ 1 Mbiri 23:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Anali kutumidwanso pa ntchito zokhudza mkate wosanjikiza,+ ufa wosalala+ wa nsembe yambewu, mikate yopyapyala+ yopanda chofufumitsa,+ makeke ophika m’chiwaya,+ ufa wokanya wosakaniza ndi mafuta,+ ndiponso miyezo yosiyanasiyana.+
21 Nsembeyo ikhale yosakaniza ndi mafuta, yophika m’chiwaya.+ Ikhale yosakaniza bwino ndi mafuta. Upereke mitanda ya nsembe yambewu monga fungo lokhazika mtima pansi kwa Yehova.
9 “‘Nsembe iliyonse yambewu imene ingaphikidwe mu uvuni,+ iliyonse yophika mu mphika wa mafuta ambiri+ ndiponso yophika m’chiwaya+ izikhala ya wansembe amene wapereka nsembeyo. Ndithu izikhala yake.+
29 Anali kutumidwanso pa ntchito zokhudza mkate wosanjikiza,+ ufa wosalala+ wa nsembe yambewu, mikate yopyapyala+ yopanda chofufumitsa,+ makeke ophika m’chiwaya,+ ufa wokanya wosakaniza ndi mafuta,+ ndiponso miyezo yosiyanasiyana.+