Levitiko 24:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndipo usanjikize mikateyo m’magulu awiri. Gulu lililonse likhale ndi mikate 6.+ Uike mikateyo patebulo lagolide woyenga bwino pamaso pa Yehova.+ 1 Mbiri 9:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ena mwa ana a Akohati, abale awo, anali oyang’anira mikate yosanjikiza,+ kuti aziikonza sabata ndi sabata.+
6 Ndipo usanjikize mikateyo m’magulu awiri. Gulu lililonse likhale ndi mikate 6.+ Uike mikateyo patebulo lagolide woyenga bwino pamaso pa Yehova.+
32 Ena mwa ana a Akohati, abale awo, anali oyang’anira mikate yosanjikiza,+ kuti aziikonza sabata ndi sabata.+