Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 40:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Kenako anasanja mkate woonetsa+ Yehova patebulopo, monga mmene Yehova analamulira Mose.

  • 1 Samueli 21:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Koma wansembeyo anayankha Davide kuti: “Ndilibe mkate wamba, koma pali mkate wopatulika.+ Nditha kukupatsa umenewu ngati anyamatawo ayesetsa kudzisunga osagona ndi akazi.”+

  • Maliko 2:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 M’nkhani yonena za Abiyatara+ wansembe wamkulu, Davide analowa m’nyumba ya Mulungu ndi kudya mitanda ya mkate woonetsa+ kwa Mulungu. Anatenga mitanda ina ya mkatewo n’kupatsanso amuna amene anali naye limodzi.+ Oyenera kudya mkate umenewu ndi ansembe okha basi ndipo anthu ena onse saloledwa kudya.+ Kodi inu simunawerenge nkhani imeneyi?”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena