Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 25:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Ndipo patebulopo uziikapo mkate wachionetsero pamaso panga nthawi zonse.+

  • Levitiko 24:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 “Ndiyeno utenge ufa wosalala ndi kuphika mikate 12 yozungulira yoboola pakati. Mkate uliwonse uzipangidwa ndi ufa wokwanira magawo awiri mwa magawo 10 a muyezo wa efa.

  • Levitiko 24:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Mkatewo uzikhala wa Aroni ndi ana ake,+ ndipo aziudyera m’malo oyera,+ chifukwa wapatsidwa kwa iye monga chinthu choyera koposa kuchokera pa nsembe zotentha ndi moto zoperekedwa kwa Yehova. Limeneli likhale lamulo mpaka kalekale.”

  • Mateyu 12:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Kodi sanalowe m’nyumba ya Mulungu ndi kudya mitanda ya mkate woonetsa kwa Mulungu,+ umene iye ndi anthu omwe anali nawo aja sanayenera kudya malinga ndi malamulo,+ koma ansembe okha?+

  • Luka 6:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Kodi simunawerenge kuti analowa m’nyumba ya Mulungu ndi kutenga mitanda ya mkate woonetsa kwa Mulungu+ n’kudya, ndipo ina anapatsa amuna amene anali naye limodzi? Malamulo salola aliyense kudya mkate umenewu koma ansembe okha.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena