Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 21:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Iye angadye mkate wa Mulungu wake kuchokera pa zinthu zopatulika koposa+ ndi pa zinthu zopatulika.+

  • Levitiko 22:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 “‘Munthu wamba* asadye chopatulika chilichonse.+ Mlendo wokhala m’nyumba ya wansembe kapena munthu waganyu, asadye chopatulika chilichonse.

  • 1 Samueli 21:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Pamenepo wansembeyo anam’patsa mkate wopatulika,+ chifukwa panalibe mkate wina koma mkate wachionetsero wokha, umene anali atauchotsa pamaso pa Yehova+ pa tsiku limenelo kuti aikepo watsopano.

  • Mateyu 12:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Kodi sanalowe m’nyumba ya Mulungu ndi kudya mitanda ya mkate woonetsa kwa Mulungu,+ umene iye ndi anthu omwe anali nawo aja sanayenera kudya malinga ndi malamulo,+ koma ansembe okha?+

  • Luka 6:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Kodi simunawerenge kuti analowa m’nyumba ya Mulungu ndi kutenga mitanda ya mkate woonetsa kwa Mulungu+ n’kudya, ndipo ina anapatsa amuna amene anali naye limodzi? Malamulo salola aliyense kudya mkate umenewu koma ansembe okha.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena