Ekisodo 25:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ndipo patebulopo uziikapo mkate wachionetsero pamaso panga nthawi zonse.+ Ekisodo 29:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ndipo Aroni ndi ana ake adye+ nyama ya nkhosayo ndi mkate umene uli m’dengu, adyere pakhomo la chihema chokumanako. Levitiko 24:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mkatewo uzikhala wa Aroni ndi ana ake,+ ndipo aziudyera m’malo oyera,+ chifukwa wapatsidwa kwa iye monga chinthu choyera koposa kuchokera pa nsembe zotentha ndi moto zoperekedwa kwa Yehova. Limeneli likhale lamulo mpaka kalekale.”
32 Ndipo Aroni ndi ana ake adye+ nyama ya nkhosayo ndi mkate umene uli m’dengu, adyere pakhomo la chihema chokumanako.
9 Mkatewo uzikhala wa Aroni ndi ana ake,+ ndipo aziudyera m’malo oyera,+ chifukwa wapatsidwa kwa iye monga chinthu choyera koposa kuchokera pa nsembe zotentha ndi moto zoperekedwa kwa Yehova. Limeneli likhale lamulo mpaka kalekale.”