Ekisodo 25:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ndipo patebulopo uziikapo mkate wachionetsero pamaso panga nthawi zonse.+ Levitiko 24:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Sabata lililonse azikhazika mkatewo pamaso pa Yehova, ndipo uzikhala pamenepo nthawi zonse.+ Limeneli ndi pangano pakati pa ine ndi ana a Isiraeli mpaka kalekale. 1 Samueli 21:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pamenepo wansembeyo anam’patsa mkate wopatulika,+ chifukwa panalibe mkate wina koma mkate wachionetsero wokha, umene anali atauchotsa pamaso pa Yehova+ pa tsiku limenelo kuti aikepo watsopano.
8 Sabata lililonse azikhazika mkatewo pamaso pa Yehova, ndipo uzikhala pamenepo nthawi zonse.+ Limeneli ndi pangano pakati pa ine ndi ana a Isiraeli mpaka kalekale.
6 Pamenepo wansembeyo anam’patsa mkate wopatulika,+ chifukwa panalibe mkate wina koma mkate wachionetsero wokha, umene anali atauchotsa pamaso pa Yehova+ pa tsiku limenelo kuti aikepo watsopano.