1 Mbiri 6:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ana a Merari anali Mali ndi Musi.+ Mabanja a Alevi potsatira mayina a makolo awo ndi awa:+