1 Mbiri 26:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Hosa, wochokera mwa ana a Merari anali ndi ana. Simuri anali mtsogoleri wa anawo ngakhale kuti sanali woyamba kubadwa,+ koma bambo akewo ndiwo anamusankha kukhala mtsogoleri.+
10 Hosa, wochokera mwa ana a Merari anali ndi ana. Simuri anali mtsogoleri wa anawo ngakhale kuti sanali woyamba kubadwa,+ koma bambo akewo ndiwo anamusankha kukhala mtsogoleri.+