1 Mbiri 29:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Miyala iliyonse yamtengo wapatali imene munthu aliyense anali nayo, anaipereka ku chuma cha panyumba ya Yehova, chomwe Yehiela+ Mgerisoni+ anali kuyang’anira.
8 Miyala iliyonse yamtengo wapatali imene munthu aliyense anali nayo, anaipereka ku chuma cha panyumba ya Yehova, chomwe Yehiela+ Mgerisoni+ anali kuyang’anira.