Numeri 31:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Monga msonkho+ kwa Yehova, pa gawo loperekedwa kwa asilikali omwe anapita kunkhondo, mutengepo chamoyo chimodzi pa zamoyo 500 zilizonse, pa anthu, ng’ombe, abulu, ndi nkhosa.
28 Monga msonkho+ kwa Yehova, pa gawo loperekedwa kwa asilikali omwe anapita kunkhondo, mutengepo chamoyo chimodzi pa zamoyo 500 zilizonse, pa anthu, ng’ombe, abulu, ndi nkhosa.