1 Samueli 16:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kenako Jese anaitana Shama+ kuti adutse, koma Samueli anati: “Yehova sanasankhenso ameneyu.” 1 Mbiri 20:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iye anali kutonza ndi kuderera+ Isiraeli, ndipo pamapeto pake Yonatani mwana wa Simeya,+ m’bale wake wa Davide, anamupha.
7 Iye anali kutonza ndi kuderera+ Isiraeli, ndipo pamapeto pake Yonatani mwana wa Simeya,+ m’bale wake wa Davide, anamupha.