Deuteronomo 32:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ngati ndikanati sindikuopa kusautsidwa ndi mdani,+Kuti adani awo angamve molakwa,+Kutinso anganene kuti: “Dzanja lathu lapambana,+Ndipo si Yehova amene wachita zonsezi.”+ 1 Samueli 17:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiyeno Mfilisiti uja anapitiriza kunena kuti: “Ine ndikutonza+ asilikali a Isiraeli lero. Ndipatseni mwamuna woti ndimenyane naye!”+ 2 Mafumu 19:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kodi ndani amene iwe wamutonza+ ndi kumulankhula monyoza?+Ndipo ndani amene iwe wam’kwezera mawu,+Ndi kum’kwezera maso ako m’mwamba?+Ndi Woyera wa Isiraeli!+
27 Ngati ndikanati sindikuopa kusautsidwa ndi mdani,+Kuti adani awo angamve molakwa,+Kutinso anganene kuti: “Dzanja lathu lapambana,+Ndipo si Yehova amene wachita zonsezi.”+
10 Ndiyeno Mfilisiti uja anapitiriza kunena kuti: “Ine ndikutonza+ asilikali a Isiraeli lero. Ndipatseni mwamuna woti ndimenyane naye!”+
22 Kodi ndani amene iwe wamutonza+ ndi kumulankhula monyoza?+Ndipo ndani amene iwe wam’kwezera mawu,+Ndi kum’kwezera maso ako m’mwamba?+Ndi Woyera wa Isiraeli!+