Deuteronomo 31:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Sonkhanitsani akulu onse a mafuko anu ndi atsogoleri anu,+ kuti ndilankhule mawu awa m’makutu mwawo, ndipo nditenge kumwamba ndi dziko lapansi kukhala mboni zanga pamaso pawo.+ Yoswa 23:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pa nthawiyo, Yoswa anaitana Aisiraeli onse+ ndi akulu awo, omwe anali atsogoleri awo, oweruza awo, ndi akapitawo awo,+ n’kuwauza kuti: “Ine ndakalamba ndipo ndili ndi zaka zambiri.
28 Sonkhanitsani akulu onse a mafuko anu ndi atsogoleri anu,+ kuti ndilankhule mawu awa m’makutu mwawo, ndipo nditenge kumwamba ndi dziko lapansi kukhala mboni zanga pamaso pawo.+
2 Pa nthawiyo, Yoswa anaitana Aisiraeli onse+ ndi akulu awo, omwe anali atsogoleri awo, oweruza awo, ndi akapitawo awo,+ n’kuwauza kuti: “Ine ndakalamba ndipo ndili ndi zaka zambiri.