1 Samueli 8:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Idzatenganso gawo limodzi mwa magawo 10+ a zokolola za m’minda yanu ya mbewu ndi ya mpesa, n’kuzipereka kwa nduna za panyumba ya mfumu+ ndi kwa antchito ake.
15 Idzatenganso gawo limodzi mwa magawo 10+ a zokolola za m’minda yanu ya mbewu ndi ya mpesa, n’kuzipereka kwa nduna za panyumba ya mfumu+ ndi kwa antchito ake.