Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mbiri 27:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Tsopano nawa magulu a Aisiraeli amene anali m’gulu la asilikali a mfumu. M’magulu amenewa munali atsogoleri a nyumba za makolo awo,+ atsogoleri+ a magulu a anthu 1,000, atsogoleri a magulu a anthu 100,+ ndi atsogoleri amene anali kusamalira magulu amenewa. Maguluwa anali kusinthanasinthana mwezi uliwonse pa chaka kutumikira+ mfumu, ndipo gulu lililonse linali ndi anthu 24,000.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena