2 Mbiri 20:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 n’kunena kuti:+ “Inu Yehova Mulungu wa makolo athu,+ kodi si inu Mulungu wakumwamba?+ Kodi inu simukulamulira maufumu onse a mitundu ya anthu?+ Kodi m’dzanja lanu si muli mphamvu kotero kuti palibe amene angalimbane nanu?+
6 n’kunena kuti:+ “Inu Yehova Mulungu wa makolo athu,+ kodi si inu Mulungu wakumwamba?+ Kodi inu simukulamulira maufumu onse a mitundu ya anthu?+ Kodi m’dzanja lanu si muli mphamvu kotero kuti palibe amene angalimbane nanu?+