Numeri 32:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Noba nayenso ananyamuka ulendo wokalanda mzinda wa Kenati+ ndi midzi yake yozungulira. Mzindawo anaupatsa dzina lake, loti Noba.
42 Noba nayenso ananyamuka ulendo wokalanda mzinda wa Kenati+ ndi midzi yake yozungulira. Mzindawo anaupatsa dzina lake, loti Noba.