2 Mafumu 21:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Amoni+ anali ndi zaka 22 pamene anayamba kulamulira, ndipo analamulira zaka ziwiri+ ku Yerusalemu. Mayi ake anali a ku Yotiba, ndipo dzina lawo linali Mesulemeti mwana wa Haruzi.
19 Amoni+ anali ndi zaka 22 pamene anayamba kulamulira, ndipo analamulira zaka ziwiri+ ku Yerusalemu. Mayi ake anali a ku Yotiba, ndipo dzina lawo linali Mesulemeti mwana wa Haruzi.