1 Mbiri 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Manase anabereka Amoni,+ ndipo Amoni anabereka Yosiya.+ Mateyu 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Hezekiya anabereka Manase.+Manase+ anabereka Amoni.+Amoni+ anabereka Yosiya.