2 Mafumu 22:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Yosiya+ anali ndi zaka 8 pamene anayamba kulamulira, ndipo analamulira zaka 31 ku Yerusalemu. Mayi ake anali a ku Bozikati.+ Dzina lawo linali Yedida mwana wa Adaya. Mateyu 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Hezekiya anabereka Manase.+Manase+ anabereka Amoni.+Amoni+ anabereka Yosiya.
22 Yosiya+ anali ndi zaka 8 pamene anayamba kulamulira, ndipo analamulira zaka 31 ku Yerusalemu. Mayi ake anali a ku Bozikati.+ Dzina lawo linali Yedida mwana wa Adaya.