Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 13:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Ndiyeno anafuulira guwa lansembelo mawu ochokera kwa Yehova oitanira tsoka, kuti: “Guwa lansembe iwe! Guwa lansembe iwe! Yehova wanena kuti, ‘Mwana wamwamuna adzabadwa m’nyumba ya Davide, dzina lake Yosiya.+ Ndithu adzatenga ansembe a malo okwezeka amene akufukiza nsembe yautsi pa iwe, n’kuwapereka nsembe pa iwe. Iye adzawotcha mafupa a anthu pa iwe.’”+

  • 1 Mbiri 3:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Manase anabereka Amoni,+ ndipo Amoni anabereka Yosiya.+

  • 2 Mbiri 34:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Yosiya+ anali ndi zaka 8+ pamene anayamba kulamulira, ndipo analamulira zaka 31 ku Yerusalemu.+

  • Yeremiya 1:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Yeremiya analandira mawu ochokera kwa Yehova m’masiku a Yosiya+ mwana wa Amoni.+ Yosiya anali mfumu ya Yuda, ndipo Yeremiya analandira mawuwo m’chaka cha 13 cha ulamuliro wa Yosiyayo.+

  • Zefaniya 1:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 1 M’masiku a Yosiya+ mwana wa Amoni+ mfumu ya Yuda, Yehova analankhula kudzera mwa Zefaniya mwana wa Kusa, mwana wa Gedaliya, mwana wa Amariya, mwana wa Hezekiya. Iye anati:

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena