2 Mafumu 22:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Yosiya+ anali ndi zaka 8 pamene anayamba kulamulira, ndipo analamulira zaka 31 ku Yerusalemu. Mayi ake anali a ku Bozikati.+ Dzina lawo linali Yedida mwana wa Adaya. Yeremiya 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yeremiya analandira mawu ochokera kwa Yehova m’masiku a Yosiya+ mwana wa Amoni.+ Yosiya anali mfumu ya Yuda, ndipo Yeremiya analandira mawuwo m’chaka cha 13 cha ulamuliro wa Yosiyayo.+
22 Yosiya+ anali ndi zaka 8 pamene anayamba kulamulira, ndipo analamulira zaka 31 ku Yerusalemu. Mayi ake anali a ku Bozikati.+ Dzina lawo linali Yedida mwana wa Adaya.
2 Yeremiya analandira mawu ochokera kwa Yehova m’masiku a Yosiya+ mwana wa Amoni.+ Yosiya anali mfumu ya Yuda, ndipo Yeremiya analandira mawuwo m’chaka cha 13 cha ulamuliro wa Yosiyayo.+