-
Yoswa 15:58Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
58 Haluli, Beti-zuri, Gedori,
-
-
1 Mbiri 4:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Mkazi wake wachiyuda anabereka Yeredi bambo wa Gedori, Hiberi bambo wa Soko, ndi Yekutieli bambo wa Zanowa. Amenewa anali ana a Bitiya mwana wamkazi wa Farao, amene Meredi anam’kwatira.
-