Miyambo 15:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mwana wanzeru ndi amene amakondweretsa bambo ake,+ koma wopusa amanyoza mayi ake.+