Yoswa 15:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Otiniyeli+ mwana wa Kenazi,+ m’bale wake wa Kalebe, analanda mzindawo. Chotero Kalebe anam’patsa Akisa,+ mwana wake, kuti akhale mkazi wake.
17 Otiniyeli+ mwana wa Kenazi,+ m’bale wake wa Kalebe, analanda mzindawo. Chotero Kalebe anam’patsa Akisa,+ mwana wake, kuti akhale mkazi wake.