Genesis 49:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Rubeni, iwe ndiwe mwana wanga woyamba kubadwa,+ nyonga yanga ndi poyambira mphamvu zanga zobereka.+ Unayenera kukhala ndi ulemu wopambana ndi mphamvu zopambana.
3 “Rubeni, iwe ndiwe mwana wanga woyamba kubadwa,+ nyonga yanga ndi poyambira mphamvu zanga zobereka.+ Unayenera kukhala ndi ulemu wopambana ndi mphamvu zopambana.