1 Samueli 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Tsopano panali mwamuna wina wa ku Ramatayimu-zofimu,+ kudera lamapiri la Efuraimu,+ dzina lake Elikana.+ Iye anali mwana wa Yerohamu, mwana wa Elihu, mwana wa Tohu, mwana wa Zufi+ Mwefuraimu.* 1 Mbiri 6:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Mwana wa Elikana anali Zofai,+ mwana wa Zofai anali Nahati,
1 Tsopano panali mwamuna wina wa ku Ramatayimu-zofimu,+ kudera lamapiri la Efuraimu,+ dzina lake Elikana.+ Iye anali mwana wa Yerohamu, mwana wa Elihu, mwana wa Tohu, mwana wa Zufi+ Mwefuraimu.*