Yoswa 21:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Ana a Merari,+ omwe anatsala pa mabanja a Alevi, anapatsidwa mizinda yokwana 12 potsata mabanja awo, mwa kuchita maere.
40 Ana a Merari,+ omwe anatsala pa mabanja a Alevi, anapatsidwa mizinda yokwana 12 potsata mabanja awo, mwa kuchita maere.