1 Mbiri 6:63 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 63 Ana a Merari+ potsata mabanja awo anapatsidwa mizinda kuchokera ku fuko la Rubeni,+ fuko la Gadi,+ ndi fuko la Zebuloni.+ Anapatsidwa mizinda 12 atachita maere.
63 Ana a Merari+ potsata mabanja awo anapatsidwa mizinda kuchokera ku fuko la Rubeni,+ fuko la Gadi,+ ndi fuko la Zebuloni.+ Anapatsidwa mizinda 12 atachita maere.