1 Mbiri 2:54 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 54 Ana a Salima anali anthu okhala ku Betelehemu,+ ku Netofa,+ ndi ku Atiroti-beti-yowabu. Hafu ya anthu okhala ku Manahati ndi anthu okhala ku Zora, analinso ana a Salima. Nehemiya 12:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ana aamuna a oimbawo anasonkhana pamodzi kuchokera m’Chigawo*+ chapafupi, m’madera onse ozungulira Yerusalemu komanso m’midzi yonse kumene Anetofa anali kukhala.+
54 Ana a Salima anali anthu okhala ku Betelehemu,+ ku Netofa,+ ndi ku Atiroti-beti-yowabu. Hafu ya anthu okhala ku Manahati ndi anthu okhala ku Zora, analinso ana a Salima.
28 Ana aamuna a oimbawo anasonkhana pamodzi kuchokera m’Chigawo*+ chapafupi, m’madera onse ozungulira Yerusalemu komanso m’midzi yonse kumene Anetofa anali kukhala.+